Psalms 149:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atamande Mulungu kwambiri mokweza mau, malupanga akuthwa konsekonse ali m'manja,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nyimbo zakukweza Mulungu zikhale pakamwa pao, ndi lupanga lakuthwa konsekonse m'dzanja lao;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Matamando a Mulungu akhale pakamwa pawo, ndi lupanga lakuthwa konsekonse mʼmanja mwawo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nyimbo zakukweza Mulungu zikhale pakamwa pao, Ndi lupanga lakuthwa konse konse m'dzanja lao;