Psalms 149:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
kuti alipsire mafuko achikunja, kuti alange mitundu ina ya anthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kubwezera chilango akunja, ndi kulanga mitundu ya anthu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kubwezera chilango anthu a mitundu ina, ndi kulanga anthu a mitundu yonse,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kubwezera cilango akunja, Ndi kulanga mitundu ya anthu;