Psalms 149:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
kuti aŵalange monga momwe Mulungu adalamulira. Umenewu ndiwo ulemerero wa anthu okhulupirira Chauta. Tamandani Chauta!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuwachitira chiweruzo cholembedwacho. Ulemu wa okondedwa ake onse ndi uwu. Aleluya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuchita zimene zinalembedwa zotsutsana nawo Uwu ndi ulemerero wa oyera mtima ake onse. Tamandani Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuwacitira ciweruzo colembedwaco: Ulemu wa okondedwa ace onse ndi uwu. Haleluya.