Psalms 15:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndi amene sakongoza ndalama zake kuti alandire chiwongoladzanja, amene salandira chiphuphu kuti azunze munthu wosalakwa. Munthu wochita zimenezi, palibe chilichonse chimene chidzamgwedeze.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndalama zake sakongoletsa mofuna phindu lalikulu, ndipo salandira chokometsera mlandu kutsutsa wosachimwa. Munthu wakuchita izi sadzagwedezeka kunthawi zonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
amene amakongoletsa ndalama zake popanda chiwongoladzanja ndipo salandira chiphuphu pofuna kutsutsa anthu osalakwa. Iye amene amachita zinthu zimenezi sadzagwedezeka konse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndarama zace sakongoletsa mofuna phindu lalikuru, Ndipo salandira cokometsera mlandu kutsutsa wosacimwa. Munthu wakucita izi sadzagwedezeka ku nthawi zonse,