Psalms 150:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mtamandeni chifukwa cha ntchito zake zamphamvu, mtamandeni chifukwa cha ukulu wake wopambana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mlemekezeni chifukwa cha ntchito zake zolimba; mlemekezeni monga mwa ukulu wake waunjinji.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mutamandeni chifukwa cha machitidwe ake amphamvu; mutamandeni chifukwa cha ukulu wake wopambana.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mlemekezeni cifukwa ca nchito zace zolimba; Mlemekezeni monga mwa ukulu wace waunjinji.