Psalms 16:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mundisunge Inu Mulungu, pakuti ndikuthaŵira kwa Inu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mikitamu wa Davide. Ndisungeni ine, Mulungu: pakuti ndakhulupirira Inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mikitamu ya Davide. Ndisungeni Inu Mulungu, pakuti ine ndimathawira kwa Inu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndisungeni ine, Mulungu: pakuti ndakhulupirira Inu.