Psalms 16:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
chifukwa simudzandisiya ku malo a anthu akufa, simudzalola kuti wokondedwa wanune ndikaole kumeneko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti simudzasiya moyo wanga kumanda; simudzalola wokondedwa wanu avunde.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
chifukwa Inu simudzandisiya ku manda, simudzalola kuti woyera wanu avunde.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti simudzasiya moyo wanga kumanda; Simudzalola wokondedwa wanu abvunde.