Psalms 16:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amene amasankhula milungu ina, amadzichulukitsira mavuto. Sindidzatsira nawo nsembe zao zamagazi kapena kutchula maina a milungu yaoyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Zidzachuluka zisoni zao za iwo otsata Mulungu wina. Sindidzathira nsembe zao zamwazi, ndipo sindidzatchula maina ao pakamwa panga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu amene amathamangira kwa milungu ina mavuto awo adzachulukadi. Ine sindidzathira nawo nsembe zawo zamagazi kapena kutchula mayina awo ndi pakamwa panga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Zidzacuruka zisoni zao za iwo otsata mulungu wina: Sindidzathira nsembe zao zamwazi, Ndipo sindidzachula maina ao pakamwa panga,