Psalms 16:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake mtima wanga ukukondwa, ndipo m'katikati mwangamu ndikusangalala. Thupi langanso lidzakhala pabwino,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake wasekera mtima wanga, nukondwera ulemu wanga; mnofu wanganso udzakhala mokhazikika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho mtima wanga ndi wosangalala ndipo pakamwa panga pakukondwera; thupi langanso lidzakhala pabwino,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace wasekera mtima wanga, nukondwera ulemu wanga; Mnofu wanganso udzakhala mokhazikika.