Psalms 17:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mitima yao ilibe chifundo, amalankhula modzikuza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mafuta ao awatsekereza; m'kamwa mwao alankhula modzikuza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo amatseka mitima yawo yopanda chifundo, ndi pakamwa pawo amayankhula modzitamandira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mafuta ao awatsekereza; M'kamwa mwao alankhula modzikuza.