Psalms 17:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ali ngati mkango wofunitsitsa kuti ukadzule, ngati chilombo cholusa cholalira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Afanana ndi mkango wofuna kumwetula, ndi msona wa mkango wakukhala mobisalamo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo ali ngati mkango wofuna nyama; ngati mkango waukulu wokhala mobisala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Afanana ndi mkango wofuna kumwetula, Ndi msona wa mkango wakukhala mobisalamo.