Psalms 17:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ine m'kulungama kwanga ndidzaona nkhope yanu. Tsono ine nditadzuka, ndidzakondwa kotheratu poonana ndi Inu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ine ndidzapenyerera nkhope yanu m'chilungamo, ndidzakhuta mtima ndi maonekedwe anu, pamene ndidzauka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo ine mʼchilungamo ndidzaona nkhope yanu; pamene ndidzadzuka, ndidzakondwera kwambiri poonana nanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ine ndidzapenyerera nkhope yanu m'cilungamo: Ndidzakhuta mtima ndi maonekedwe anu, pamene ndidzauka.