Psalms 17:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngakhale muyese mtima wanga, kapena kundipenyetsetsa usiku, kaya mundiyang'anitsitse chotani, mudzapeza kuti ndilibe mlandu. Pakamwa panga sipalankhula zoipa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwayesera mtima wanga; mwandizonda usiku; mwandisuntha, simupeza kanthu; mwatsimikiza mtima kuti m'kamwa mwanga simudzalakwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngakhale Inu mutafufuza mtima wanga ndi kundisanthula usiku, ngakhale mutandiyesa, simudzapeza kanthu; Ine ndatsimikiza kuti pakamwa panga sipadzachimwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwayesera mtima wanga; mwandizonda usiku; Mwandisuntha, simupeza kanthu; Ndatsimikiza mtima kuti m'kamwa mwanga simudzalakwa.