Psalms 17:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kunena za ntchito za anthu, ine posunga mau anu, sindidatsate za anthu andeu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Za machitidwe a anthu, ndachenjera ndi mau a milomo yanu ndingalowe njira za woononga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kunena za ntchito za anthu, monga mwa mawu a pakamwa panu, Ine ndadzisunga ndekha posatsata njira zachiwawa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Za macitidwe a anthu, ndaceniera ndi mau a milomo yanu Ndingalowe njira za woononga.