Psalms 17:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mundisunge ngati mwana wa diso, munditeteze pansi pa mapiko anu,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndisungeni monga kamwana ka m'diso, ndifungatireni mu mthunzi wa mapiko anu,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mundisunge ine ngati mwanadiso; mundibise mu mthunzi wa mapiko anu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndisungeni monga kamwana ka m'diso, Ndifungatireni mu mthunzi wa mapiko anu,