Psalms 17:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
kuti asandiwone anthu oipa ofuna kupasula, ndiye kuti adani anga oopsaŵa amene akundizinga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kundilanditsa kwa oipa amene andipasula, adani a pa moyo wanga amene andizinga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuchoka kwa oyipa amene amandizinga ine, kuchoka kwa anthu amene ndi adani anga, amene andizungulira ine.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kundilanditsa kwa oipa amene andipasula, Adani a pa moyo wanga amene andizinga.