Psalms 18:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndimakukondani Chauta, Inu mphamvu zanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kwa Mkulu wa Nyimbo. Salimo la Davide, mtumiki wa Yehova, amene ananena kwa Yehova mau a nyimbo iyi m'mene Yehova anamlanditsa m'dzanja la adani ake onse, ndi m'dzanja la Saulo: ndipo anati, Ndikukondani, Yehova, mphamvu yanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kwa mtsogoleri wa mayimbidwe. Salimo la Davide mtumiki wa Yehova. Iye anayimbira Yehova nyimbo iyi pamene Yehovayo anamupulumutsa mʼdzanja la adani ake onse ndiponso mʼdzanja la Sauli. Davide anati: Ine ndimakukondani Inu Yehova, mphamvu zanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndikukondani, Yehova, mphamvu yanga.