Psalms 18:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mdima adausandutsa chofunda chake, mitambo yakuda yamvula adaisandutsa mwafuli wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anaika mdima pobisala pake, hema wake womzinga; mdima wa madzi, makongwa a kuthambo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anapanga mdima kukhala chofunda chake, chophimba chake chomuzungulira chinali mitambo yakuda ya mlengalenga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anaika mdima pobisala pace, hema wace womzinga; Mdima wa madzi, makongwa a kuthambo.