Psalms 18:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'kuŵala kumene kunali pamaso pake, munkafumira matalala ndi makala amoto, amene adabzola mitambo yophimba ija.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwa kuchezemira kunali pamaso pake makongwa anakanganuka, matalala ndi makala amoto.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼkuwala kumene kunali pamaso pake munkachokera matalala, makala amoto ndi ziphaliwali zongʼanima.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwa kucezemira kunali pamaso pace makongwa anakanganuka, Matalala ndi makala amoto.