Psalms 18:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adaponya mivi yake nabalalitsa adani ake, adachititsa zing'aning'ani, naŵapirikitsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anatuma mivi yake nawabalalitsa; inde mphezi zaunyinji, nawamwaza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anaponya mivi yake nabalalitsa adani ake, ndi zingʼaningʼani zake anawagonjetsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anatuma mibvi yace nawabalalitsa; Inde mphezi zaunyinji, nawamwaza.