Psalms 18:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngalande zozama zam'nyanja zidaonekera, maziko a dziko lapansi adakhala poyera, pamene Inu Chauta mudakhuluma mokalipa, pamene mudatulutsa mpweya wamphamvu m'mphuno mwanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo zidaoneka zoyendamo madzi, nafukuka maziko a dziko lapansi, mwa kudzudzula kwanu, Yehova, mwa mpumo wa mpweya wa m'mphuno mwanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zigwa za mʼnyanja zinaonekera poyera; maziko a dziko lapansi anakhala poyera, Yehova atabangula mwaukali, pamene mpweya wamphamvu unatuluka mʼmphuno mwanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo zidaoneka zoyendamo madzi, Nafukuka maziko a dziko lapansi, Mwa kudzudzula kwanu, Yehova, Mwa mpumo wa mpweya wa m'mphuno mwanu.