Psalms 18:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adandipulumutsa kwa adani anga amphamvu, kwa onse amene ankadana nane, pakuti iwo anali amphamvu kwambiri kupambana ine.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anandipulumutsa ine kwa mdani wanga wamphamvu, ndi kwa iwo ondida ine, pakuti anandiposa mphamvu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anandipulumutsa kwa mdani wanga wamphamvu, adani anga, amene anali amphamvu kuposa ine.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anandipulumutsa ine kwa mdani wanga wamphamvu, Ndi kwa iwo ondida ine, pakuti anandiposa mphamvu.