Psalms 18:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adandipatsa mphotho molingana ndi ntchito zanga zabwino, adandifupa molingana ndi ungwiro wanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova anandibwezera monga mwa chilungamo changa; anandisudzula monga mwa kusisira kwa manja anga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova wandithandiza molingana ndi chilungamo changa; molingana ndi makhalidwe anga abwino, Iye wandipulumutsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova anandibwezera monga mwa cilungamo canga; Anandisudzula monga mwa kusisira kwa manja anga.