Psalms 18:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ine ndidatsata njira za Chauta, sindidachite zoipa ndi kumsiya Mulungu wanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ndasunga njira za Yehova, ndipo sindinachitira choipa kusiyana ndi Mulungu wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti ine ndinatsata njira za Yehova; ndilibe mlandu wochoka pamaso Mulungu wanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ndasunga njira za Yehova, Ndipo sindinacitira coipa kusiyana ndi Mulungu wanga.