Psalms 18:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndinalibe mlandu pamaso pake, ndinkalewa zoipa m'moyo mwanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndinakhala wangwiro ndi Iye, ndipo ndinadzisunga wosachita choipa changa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndakhala moyo wosalakwa pamaso pake ndipo ndakhala ndi kupewa tchimo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndinakhala wangwiro ndi iye, Ndipo ndinadzisunga wosacita coipa canga.