Psalms 18:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake Chauta wandipatsa mphotho molingana ndi ntchito zanga zabwino, monga momwe akuwonera kuti ndilibe mlandu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndimo anandisudzulira Yehova monga mwa chilungamo changa, monga mwa kusisira kwa manja anga pamaso pake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova wandipatsa mphotho molingana ndi chilungamo changa, molingana ndi kuyera kwa manja anga pamaso pake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndimo anandisudzulira Yehova monga mwa cilungamo canga, Monga mwa kusisira kwa manja anga pamaso pace.