Psalms 18:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kwa anthu okhulupirika, Inu Mulungu mumadziwonetsa okhulupirika. Kwa anthu aungwiro, mumadziwonetsa abwino kotheratu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pa wachifundo mukhala wachifundo; pa munthu wangwiro mukhala wangwiro.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kwa wokhulupirika, Inu mumaonetsa kukhulupirika kwanu; kwa anthu amakhalidwe abwino, Inu mumaonetsanso makhalidwe abwino,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pa wacifundo mukhala wacifundo Pa mumthu wangwiro mukhala wangwiro;