Psalms 18:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kwa anthu oyera mtima mumadziwonetsa okoma mtima, koma kwa anthu oipa mtima, mumawonetsa kunyansidwa nawo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pa woyera mtima mukhala woyera mtima; pa wotsutsatsutsa mukhala wotsutsana naye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kwa woyera mtima, Inu mumaonetsa kuyera mtima kwanu, koma kwa achinyengo mumaonetsanso kunyansidwa nawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pa woyera mtima mukhala woyera mtima; Pa wotsutsatsutsa mukhala wotsutsana naye.