Psalms 18:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndimaitana Chauta, amene ayenera kumtamanda, ndipo amandipulumutsa kwa adani anga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndidzaitanira Yehova, woyenera kutamandika, ndipo adzandipulumutsa ine kwa adani anga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndimayitana Yehova amene ndi woyenera matamando, ndipo ndapulumutsidwa kwa adani anga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidzaitanira Yehova, woyenera kutamandika: Ndipo adzandipulumutsa ine kwa adani anga.