Psalms 18:32 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu wathu ndiye amene amandiveka mphamvu, wandichotsera zoopsa m'njira zanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mulungu ndiye wondizingiza mphamvu m'chuuno, nakonza njira yanga ikhale yangwiro.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndi Mulungu amene anandipatsa mphamvu ndi kulungamitsa njira yanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mulungu ndiye wondizingiza mphamvu m'cuuno, Nakonza njira yanga ikhale yangwiro.