Psalms 18:34 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amaphunzitsa manja anga kamenyedwe ka nkhondo, kotero kuti ndingathe kupinda uta wachitsulo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Aphunzitsa manja anga agwire nkhondo; kuti walifuka uta wamkuwa ndi manja anga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye amaphunzitsa manja anga kuchita nkhondo; manja anga amatha kuthyola uta wachitsulo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Aphunzitsa manja anga agwire nkhondo; Kuti walifuka uta wamkuwa ndi manja anga.