Psalms 18:39 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja ndinu mudandipatsa mphamvu zomenyera nkhondo, ndinu mudandigonjetsera anthu ondiwukira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti mwandizingiza mphamvu m'chuuno ku nkhondoyo; mwandigonjetsera amene andiukira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu munandiveka ndi mphamvu yokachitira nkhondo, munachititsa kuti ndigonjetse adani anga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti mwaudizingiza mphamvu m'cuuno ku nkhondoyo: Mwandigonjetsera amene andiukira.