Psalms 18:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nthambo za imfa zidandizungulira, mitsinje yothamanga yoononga idandisefukira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Zingwe za imfa zinandizinga, ndipo mitsinje ya zopanda pake inandiopsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zingwe za imfa zinandizinga; mitsinje yothamanga yachiwonongeko inandiopsa kwambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Zingwe za imfa zinandizinga, Ndipo mitsinje ya zopanda pace inandiopsa.