Psalms 18:40 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mudapirikitsa adani anga kuti andithaŵe, amene ankadana nane ndidaŵaononga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo adani anga mwawalozetsa m'mbuyo kwa ine, kuti ndipasule ondidawo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu munachititsa adani anga kutembenuka, kuonetsa misana yawo pothawa, ndipo ine ndinawononga adani angawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo adani anga mwawalozetsa m'mbuyo kwa ine, Kuti ndipasule ondidawo.