Psalms 18:41 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adakuwa kuti ena aŵathandize, koma panalibe woŵapulumutsa. Adalirira Chauta, koma sadaŵayankhe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anafuula, koma panalibe wopulumutsa; ngakhale kwa Yehova, koma sanawavomereze.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anafuwula kupempha thandizo, koma panalibe ndi mmodzi yemwe owapulumutsa. Analirira kwa Yehova koma sanawayankhe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anapfuula, koma panalibewopulumutsa; Ngakhale kwa Yehova, koma sanawabvomereza.