Psalms 18:43 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mudandipulumutsa kwa anthu olimbana nane, Inu mudandisandutsa mfumu ya mitundu yonse. Choncho anthu osaŵadziŵa ankanditumikira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwandipulumutsa pa zolimbana nane za anthu; mwandiika mutu wa amitundu; mtundu wa anthu sindinaudziwa udzanditumikira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu mwandipulumutsa mʼmanja mwa anthu; mwandisandutsa kukhala mtsogoleri wa anthu a mitundu ina. Anthu amene sindikuwadziwa ali pansi pa ulamuliro wanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwandipulumutsa pa zolimbana nane za anthu; Mwandiika mutu wa amitundu; Mtundu wa anthu sindinaudziwa udzanditumikira.