Psalms 18:46 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta ndi wamoyo. Litamandike thanthwe langa, alemekezeke Mulungu wondipulumutsa,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova ngwa moyo; ndipo lidalitsike thanthwe langa; nakwezeke Mulungu wa chipulumutso changa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova ndi wamoyo! Litamandidwe Thanthwe langa! Akuzike Mulungu Mpulumutsi wanga!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova ngwa moyo; ndipo lidalitsike thanthwe langa; Nakwezeke Mulungu wa cipulumutso canga: