Psalms 18:47 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu ndiye adandithandiza kuti ndilipsire, adagonjetsa anthu a mitundu ina, kuti akhale mu ulamuliro wanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndiye Mulungu amene andibwezerera chilango, nandigonjetsera mitundu ya anthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye ndi Mulungu amene amabwezera chilango, amene amagonjetsa anthu a mitundu yonse amene ali pansi pa ulamuliro wanga,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndiye Mulungu amene andibwe, zerera cilango, Nandigonjetsera mitundu ya anthu.