Psalms 18:48 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndiye amene adandipulumutsa kwa adani anga. Zoonadi Inu mudandikweza pamwamba pa ondiwukira, mudandilanditsa kwa anthu ankhanza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Andipulumutsa kwa adani anga. Inde mundikweza pa iwo akundiukira ine, mundikwatula kwa munthu wachiwawa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
amene amandipulumutsa mʼmanja mwa adani anga. Inu munandikuza kuposa adani anga; munandilanditsa mʼmanja mwa anthu ankhanza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Andipulumutsa kwa adani anga: Inde mundikweza pa iwo akundiukira ine: Mundikwatula kwa munthu waciwawa.