Psalms 18:49 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwa cha zimenezi ndidzakutamandani Inu Chauta, pakati pa mitundu ya anthu, ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake Yehova ndidzakuyamikani mwa amitundu, ndipo dzina lanu ndidzaliimbira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho ine ndidzakutamandani pakati pa anthu a mitundu ina, Inu Yehova; ndidzayimba nyimbo zotamanda dzina lanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace Yehova ndidzakuyamikani mwa amitundu, Ndipo dzina lanu ndidzaliyimbira.