Psalms 18:50 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu amathandiza mfumu yake, kuti izipambana nthaŵi ndi nthaŵi. Amaonetsa chikondi chake chosasinthika kwa wodzozedwa wake, ndiye kuti kwa Davide ndi kwa zidzukulu zake mpaka muyaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Alanditsa mfumu yake ndi chipulumutso chachikulu; nachitira chifundo wodzozedwa wake, Davide, ndi mbumba yake, kunthawi zonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye amapereka chipambano chachikulu kwa mfumu yake; amaonetsa chikondi chosasinthika kwa wodzozedwa wake, kwa Davide ndi zidzukulu zake kwamuyaya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Alanditsa mfumu yace ndi cipulumutso cacikuru: Nacitira cifundo wodzozedwa wace, Davide, ndi mbumba yace, ku nthawi zonse.