Psalms 18:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adang'amba thambo natsika pansi, mdima wabii unali ku mapazi ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Iye anaweramitsa thambo, natsika; ndipo pansi pa mapazi ake panali mdima bii.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anangʼamba thambo natsika pansi; pansi pa mapazi ake panali mitambo yakuda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Iye anaweramitsa thambo, natsika; Ndipo pansi pa mapazi ace panali mdima bii.