Psalms 19:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mau anga ndi maganizo anga avomerezeke pamaso panu, Inu Chauta, thanthwe langa ndi mpulumutsi wanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mau a m'kamwa mwanga ndi maganizo a m'mtima wanga avomerezeke pamaso panu, Yehova, thanthwe langa, ndi Mombolo wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mawu a mʼkamwa mwanga ndi zolingalira za mu mtima mwanga zikhale zokondweretsa pamaso panu, Inu Yehova, Thanthwe langa ndi Mpulumutsi wanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mau a m'kamwa mwanga ndi maganizo a m'mtima wanga abvomerezeke pamaso panu, Yehova, thanthwe langa, ndi Mombolo wanga,