Psalms 19:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Dzuŵalo limatuluka ngati mkwati wokondwa amene akutuluka m'nyumba mwake, ndipo limayenda ndi chimwemwe ngati ngwazi yamphamvu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo lili ngati mkwati wakutuluka m'chipinda mwake, likondwera ngati chiphona kuthamanga m'njira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Dzuwa lili ngati mkwatibwi wobwera kuchokera ku nsanja yake, ngati katswiri wokondwerera kuthamanga pa mpikisano.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo liri ngati mkwati wakuturuka m'cipinda mwace, Likondwera ngati ciphona kuthamanga m'njira.