Psalms 19:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Limatuluka kuyambira ku mathero ena a thambo, ndi kuzungulira mpaka ku mathero enanso. Palibe chinthu chilichonse chotha kulewa kutentha kwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kutuluka kwake lituluka kolekezera thambo, ndipo kuzungulira kwake lifikira ku malekezero ake; ndipo kulibe kanthu kobisalira kutentha kwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Limatuluka kuyambira mbali ina ya thambo ndi kuzungulira mpaka mbali inanso; palibe chinthu chotha kupewa kutentha kwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuturuka kwace lituruka kolekezera thambo, Ndipo kuzungulira kwace lifikira ku malekezero ace: Ndipo kulibe kanthu kobisalira kutentha kwace.