Psalms 2:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Bwanji anthu akunja akufuna kuchita chiwembu? Chifukwa chiyani anthu ameneŵa akulingalira zopandapake?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Aphokoseranji amitundu, nalingiriranji anthu zopanda pake?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼchifukwa chiyani anthu a mitundu ina akufuna kuchita chiwembu? Akonzekeranji zopanda pake anthu?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Aphokoseranji amitundu. Nalingiriranji anthu zopanda pace?