Psalms 2:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tumikirani Chauta mwamantha ndi monjenjemera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tumikirani Yehova ndi mantha, ndipo kondwerani ndi chinthenthe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tumikirani Yehova mwa mantha ndi kukondwerera ulamuliro wake monjenjemera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tumikirani Yehova ndi mantha, Ndipo kondwerani ndi cinthenthe.