Psalms 2:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mfumuyo ikuti, “Ndidzalalika zimene Chauta walengeza. Adandiwuza kuti, ‘Iwe ndiwe mwana wanga, Ine lero ndakubala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndidzauza za chitsimikizo: Yehova ananena ndi Ine, Iwe ndiwe Mwana wanga; Ine lero ndakubala.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndidzalengeza zimene Yehova walamula: Iye anati kwa Ine, “Iwe ndiwe mwana wanga; lero Ine ndakhala Atate ako.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidzauza za citsimikizo: Yehova ananena ndi Ine, Iwe ndiwe Mwana wanga; Ine lero ndakubala.