Psalms 2:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tandipempha uwone, ndidzasandutsadi mitundu ya anthu kuti ikhale choloŵa chako, ndipo dziko lonse lapansi lidzakhala lako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Undifunse, ndipo ndidzakupatsa amitundu akhale cholowa chako, ndi malekezero a dziko lapansi akhale akoako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tandipempha, ndipo ndidzachititsa kuti mitundu ya anthu ikhale cholowa chako; malekezero a dziko lapansi kuti akhale chuma chako.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Undifunse, ndipo ndidzakupatsa amitundu akhale colowa cako, Ndi malekezero a dziko lapansi akhale ako ako.