Psalms 2:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Udzaŵaphwanya ndi ndodo yachitsulo, ndi kuŵatekedza zidutswazidutswa monga mbiya.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Udzawathyola ndi ndodo yachitsulo; udzawaphwanya monga mbiya ya woumba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iweyo udzawalamulira ndi ndodo yaufumu yachitsulo; udzawaphwanya zidutswazidutswa ngati zowumba zadothi.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Udzawatyola ndi ndodo yacitsulo; Udzawaphwanya monga mbiya yawoumba.